1 Ako. 16 - Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Za zopereka zothandizira akhristu anzao

1

9Pakuti pano mwai ulipo woti nkuchita zazikulu, ndiponsotu adani alipo ambiri.

10 pamodzi ndi mpingo umene umasonkhana m'nyumba mwao, akuti moni kwa inu nonse, akhristu anzao.

20Abale onse akuti moni. Mupatsane moni mwa chikondi chenicheni.

21Ineyo Paulo, ndikuchita kulemba ndekha mau aŵa akuti “Moni.”

22Ngati munthu sakonda Ambuye, akhale wotembereredwa. Maranatha! Ambuye athu, bwerani!

23Ambuye Yesu akudalitseni.

24Chikondi changa chikhale pa inu nonse, mwa Khristu Yesu.

Blog
About Us
Message
Site Map

Who We AreWhat We EelieveWhat We Do

Terms of UsePrivacy Notice

2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.

Home
Gospel
Question
Blog
Help