1 Mbi. 6 - Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Zidzukulu za Alevi

1Ana a Levi naŵa: Geresomo, Kohati, ndi Merari.

2Ana a Kohati naŵa: Amuramu, Izara, Hebroni ndi Uziyele.

3Ana a Amuramu naŵa: Aroni, Mose ndi Miriyamu. Ana a Aroni naŵa: Nadabu, Abibu, Eleazara ndi Itamara.

4Eleazara adabereka Finehasi, Finehasi adabereka Abisuwa,

5Abisuwa adabereka Buki, Buki adabereka Uzi,

6Uzi adabereka Zeraya, Zeraya adabereka Meraiyoti,

7Meraiyoti adabereka Amariya, Amariya adabereka Ahitubi,

8Ahitubi adabereka Zadoki, Zadoki adabereka Ahimaazi,

9Ahimaazi adabereka Azariya, Azariya adabereka Yohanani,

10Yohanani adabereka Azariya (ndi iyeyu uja ankatumikira za unsembe ku nyumba imene Solomoni adamanga ku Yerusalemu).

11Azariya adabereka Amariya, Amariya adabereka Ahitubi,

12Ahitubi adabereka Zadoki, Zadoki adabereka Salumu,

13Salumu adabereka Hilikiya, Hilikiya adabereka Azariya,

14Azariya adabereka Seraya, Seraya adabereka Yehozadaki.

15Ndipo Yehozadaki adagwidwa ukapolo nthaŵi imene Chauta adalola Nebukadinezara kuti agwire ukapolo anthu a ku Yuda ndi a mu Yerusalemu.

Zidzukulu zina za Levi

16 uja, ndiponso Libina pamodzi ndi mabusa ake omwe, Yatiri, Esitemowa pamodzi ndi mabusa ake omwe,

58Hileni pamodzi ndi mabusa ake omwe, Debiri pamodzi ndi mabusa ake omwe,

59Asani pamodzi ndi mabusa ake omwe, ndiponso Betesemesi pamodzi ndi mabusa ake omwe.

60Ndipo kuchotsa ku fuko la Benjamini, adaŵapatsa Geba pamodzi ndi mabusa ake omwe, Alemeti pamodzi ndi mabusa ake omwe, ndiponso Anatoti ndi mabusa ake omwe. Mizinda yao yonse, malinga ndi mabanja ao onse, inalipo khumi ndi itatu.

61Tsono adachita maele ndipo Akohati otsala adaŵagawira midzi khumi kuchokera pa fuko lahafu la Manase.

62Ageresomo, potsata mabanja ao, adaŵagawira mizinda khumi ndi itatu kuchokera pa mafuko a Isakara, Asere, Nafutali ndiponso Manase ku Basani.

63Amerari, potsata mabanja ao, adaŵagawira mizinda khumi ndi iŵiri kuchokera pa mafuko a Rubeni, Gadi ndi Zebuloni.

64Umu ndi m'mene Aisraele adapatsira Alevi mizinda ndi mabusa ake omwe.

65Atachita maele, adaŵapatsanso mizinda ija imene inali ya mafuko a Yuda, Simeoni ndi Benjamini.

66Mabanja ena a ana a Kohati adalandira mizinda kuchokera pa fuko la Efuremu.

67Mizindayo inali iyi: Sekemu, mzinda wopulumukiramo uja, pamodzi ndi mabusa ake ku dziko lamapiri la Efuremu, Gezere pamodzi ndi mabusa ake,

68Yokomeamu pamodzi ndi mabusa ake, Betehoroni pamodzi ndi mabusa ake,

69Aiyaloni pamodzi ndi mabusa ake, Gatirimoni pamodzi ndi mabusa ake.

70Koma mizinda yochokera pa fuko la Manase wakuzambwe, Anere pamodzi ndi mabusa ake, ndiponso Bileamu pamodzi ndi mabusa ake, adaipereka kwa otsala a mabanja a Kohati.

71Mizinda yochokera pa fuko la Manase wakuvuma, imene Ageresomo adalandira, ndi iyi: Golani ku Basani pamodzi ndi mabusa ake omwe ndiponso Asitaroti pamodzi ndi mabusa ake omwe.

72Yochokera pa fuko la Isakara ndi iyi: Kedesi pamodzi ndi mabusa ake omwe, Daberati pamodzi ndi mabusa ake omwe,

73Ramoti pamodzi ndi mabusa ake omwe ndiponso Anemu ndi mabusa ake omwe.

74Yochokera pa fuko la Asere ndi iyi: Masala pamodzi ndi mabusa ake omwe, Abidoni pamodzi ndi mabusa ake omwe,

75Hukoki pamodzi ndi mabusa ake omwe, ndiponso Rehobu pamodzi ndi mabusa ake omwe.

76Yochokera pa fuko la Nafutali ndi iyi: Kedesi wa ku Galilea pamodzi ndi mabusa ake omwe, Hamoni pamodzi ndi mabusa ake omwe, ndiponso Kiriyataimu: pamodzi ndi mabusa ake omwe.

77Amerari otsala adalandirako mizinda kuchokera pa fuko la Zebuloni: Rimono pamodzi ndi mabusa ake omwe, Tabori pamodzi ndi mabusa ake omwe,

78Patsidya pa mtsinje wa Yordani ku Yeriko, kuvuma kwa Yordani, mizinda yochokera pa fuko la Rubeni ndi iyi: Bezere kuchigwa pamodzi ndi mabusa ake omwe, Yaza pamodzi ndi mabusa ake omwe,

79Kedemoti pamodzi ndi mabusa ake omwe ndiponso Mefati pamodzi ndi mabusa ake omwe.

80Yochokera pa fuko la Gadi ndi iyi: Ramoti ku Giliyadi pamodzi ndi mabusa ake omwe, Mahanaimu pamodzi ndi mabusa ake omwe,

81Hesiboni pamodzi ndi mabusa ake omwe ndiponso Yazere pamodzi ndi mabusa ake omwe.

Blog
About Us
Message
Site Map

Who We AreWhat We EelieveWhat We Do

Terms of UsePrivacy Notice

2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.

Home
Gospel
Question
Blog
Help