1
49Ophunzira amene anali pafupi ndi Yesu ataona zimene zinalikudzachitika, adafunsa Yesu kuti, “Ambuye, kodi tiŵateme ndi lupanga?”
50Apo mmodzi mwa iwo adatemadi wantchito wa mkulu wa ansembe onse, mpaka kumusenga khutu la ku dzanja lamanja.
51Koma Yesu adati, “Basi, lekani zimenezi.” Atatero adakhudza khutu la munthuyo namchiritsa.
52Kenaka Yesu adalankhula nawo onse amene adaabwera kudzamugwira, akulu a ansembe ndi atsogoleri a alonda a ku Nyumba ya Mulungu, ndiponso akulu a Ayuda. Adaŵafunsa kuti, “Bwanji mwachita kunditengera malupanga ndi zibonga ngati kuti ndine chigaŵenga?
53 wamphamvuzonse.”
70Apo onse aja adati, “Tsono ndiye kutitu ndiwe Mwana wa Mulungu, ati?” Yesu adati, “Mwanena nokha kuti ndine amene.”
71Pamenepo iwo aja adati, “Tikufuniranji umboni wina? Tadzimvera tokha mau akeŵa.”
Who We AreWhat We EelieveWhat We Do
2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.