Lk. 12 - Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Yesu achenjeza za chiphamaso

1

56Inu anthu achiphamaso, mumatha kuzindikira maonekedwe a dziko lapansi ndi a kuthambo, koma bwanji simutha kuzindikira tanthauzo la zimene zikuchitika masiku omwe ano?”

Za kuyanjana ndi mnzako wamlandu(Mt. 5.25-26)

57“Bwanji simutsimikiza nokha zoyenera kuchita?

58Monga pamene ukupita ndi mnzako wamlandu kwa woweruza, uyesetse kukonza mlanduwo mukali pa njira, kuwopa kuti angakupereke kwa woweruza, woweruzayo angakakupereke kwa msilikali, ndipo msilikaliyo angakakuponye m'ndende.

59Ndithu ndikunenetsa kuti sudzatulukamo mpaka utalipira zonse.”

Blog
About Us
Message
Site Map

Who We AreWhat We EelieveWhat We Do

Terms of UsePrivacy Notice

2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.

Home
Gospel
Question
Blog
Help