1Tsono Aisraele onse adalembedwa potsata mibadwo yao m'buku la mafumu a Aisraele. Anthu a ku Yuda adaatengedwa ukapolo kunka ku Babiloni chifukwa chakuti anali osakhulupirika.
2 kuti azimkonza pasabata paliponse.
33Alevi ena akuluakulu ankayang'anira oimba nyimbo. Iwowo ankakhala m'zipinda m'Nyumba ya Chauta, osamangika ndi ntchito zina, pakuti ankatumikira usana ndi usiku.
34Onsewo anali atsogoleri a mabanja a makolo a Alevi potsata mibadwo yao, ndipo ankakhala ku Yerusalemu.
Makolo a mfumu Saulo(1 Mbi. 8.29-38)35Yeiyele amene adaamanga mzinda wa Gibiyoni, ankakhala ku Gibiyoni komweko. Mkazi wake anali Maaka.
36Mwana wake wachisamba anali Abidoni ndipo pambuyo pa iyeyo panali Zuri, Kisi, Baala, Nere, Nadabu,
37Gedori, Ahiyo, Zekariya ndi Mikiloti,
38bambo wa Simea. Tsono, monga achibale ao aja, iwoŵanso ankakhala ku Yerusalemu pamodzi ndi achibale aowo.
39Nere adabereka Kisi, Kisi adabereka Saulo, Saulo adabereka Yonatani, Malikisuwa, Abinadabu, ndi Esibaala.
40Yonatani anabereka Meribaala. Meribaala adabereka Mika.
41Ana a Mika naŵa: Pitoni, Meleki, Tareya ndi Ahazi.
42Ahazi adabereka Yara, Yara adabereka Alemeti, Azimaveti ndi Zimiri. Zimiri adabereka Moza.
43Moza adabereka Bineya, Bineya adabereka Rafaya, Rafaya adabereka Eleasa, Eleasa adabereka Azele.
44Azele anali ndi ana asanu ndi mmodzi ndipo maina ao naŵa: Azirikamu, Bokeru, Ismaele, Seyariya, Obadiya ndi Hanani. Onseŵa anali ana a Azele.
Who We AreWhat We EelieveWhat We Do
2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.