Mt. 13 - Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Fanizo la wofesa mbeu(Mk. 4.1-9; Lk. 8.4-8)

1Tsiku lomwelo Yesu adatuluka m'nyumba nakakhala pansi m'mbali mwa nyanja.

2, adayamba kuphunzitsa anthu m'nyumba yao yamapemphero. Amene ankamumva ankadabwa nkumati, “Kodi Iyeyu, nzeru zimenezi ndi mphamvuzi adazitenga kuti?

55Kodi ameneyu si mwana wa mmisiri wa matabwa uja? Kodi suja mai wake ndi Maria? Ndipo abale ake si Yakobe, Yosefe, Simoni ndi Yuda?

56Kodi suja alongo ake onse ali nafe pompano? Nanga tsono zonsezi adazitenga kuti?”

57Yoh. 4.44Choncho adakhumudwa naye. Koma Yesu adaŵauza kuti, “Mneneri amalemekezeka kwina kulikonse, kupatula kumudzi kwao ndiponso kubanja kwao.”

58Motero sadachite zamphamvu zambiri kumeneko, chifukwa cha kusakhulupirira kwa anthuwo.

Blog
About Us
Message
Site Map

Who We AreWhat We EelieveWhat We Do

Terms of UsePrivacy Notice

2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.

Home
Gospel
Question
Blog
Help