Ntc. 7 - Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Mau a Stefano

1Mkulu wa ansembe onse adafunsa Stefano kuti, “Kodi zimenezi nzoona?”

2 aja.

9

mafano amene mudaŵapanga

kuti muziŵapembedza.

Ndidzakuchotsani kukutayani kutali,

kupitirira dziko la Babele.’

44 Tsopano inuyo mudampereka kwa adani ake ndi kumupha.

53Inu mudaalandira Malamulo a Mulungu kudzera mwa angelo, komabe simudaŵasunge konse.”

Ayuda amponya miyala Stefano

54Pamene abwalo aja adamva mau a Stefanowo, adakwiya kwabasi, namchitira tsinya.

55Koma Stefano, atadzazidwa ndi Mzimu Woyera, adayang'ana kumwamba naona ulemerero wa Mulungu, ndiponso Yesu ataimirira ku dzanja lamanja la Mulungu.

56Tsono adati, “Onani! Ndikuwona Kumwamba kotsekuka, ndipo Mwana wa Munthu ataimirira ku dzanja lamanja la Mulungu.”

57Koma iwo adafuula kwambiri, natseka m'makutu mwao, namgudukira onse pamodzi.

58Adamtulutsira kunja kwa mzinda, nakamponya miyala. Mboni zidasungiza zovala zao munthu wachinyamata wina, dzina lake Saulo.

59Pamene anthuwo ankamuponya miyala, Stefano adayamba kupemphera kuti, “Ambuye Yesu, landirani mzimu wanga.”

60Ndipo adagwada pansi nafuula kwakukulu kuti, “Ambuye, musaŵaŵerengere tchimoli.” Atanena mau ameneŵa, adafa.

Blog
About Us
Message
Site Map

Who We AreWhat We EelieveWhat We Do

Terms of UsePrivacy Notice

2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.

Home
Gospel
Question
Blog
Help