Mt. 27 - Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Yesu ku bwalo la Pilato(Mk. 15.1; Lk. 23.1-2; Yoh. 18.28-32)

1M'maŵa kutacha, akulu onse a ansembe ndi akulu a Ayuda adapanga upo kuti aphe Yesu.

2Adammanga, napita naye kwa Pilato, bwanamkubwa.

Za imfa ya Yudasi(Ntc. 1.18-19)

3 Yesu aikidwa m'manda(Mk. 15.42-47; Lk. 23.50-56; Yoh. 19.38-42)

57Chisisira chitagwa, kudafika munthu wina wolemera, wochokera ku Arimatea, dzina lake Yosefe. Nayenso anali wophunzira wa Yesu.

58Iyeyu adakapempha mtembo wa Yesu kwa Pilato. Pilato adalamula kuti ampatse mtembowo.

59Tsono Yosefe adautenga, naukulunga m'nsalu yoyera yabafuta.

60Adakauika m'manda ake atsopano ochita chosema m'thanthwe. Tsono adagubuduzira chimwala pa khomo kuti atseke pamandapo, nachoka.

61Maria wa ku Magadala ndi Maria wina uja anali pomwepo atakhala pansi kuyang'anana ndi mandawo.

Aika alonda pa manda a Yesu

62M'maŵa mwake, litapita tsiku lokonzekera Sabata, akulu a ansembe pamodzi ndi Afarisi adasonkhana napita kwa Pilato.

63Mt. 16.21; 17.23; 20.19; Mk. 8.31; 9.31; 10.33, 34; Lk. 9.22; 18.31-33Adamuuza kuti, “Bwana, tikukumbukira kuti munthu wonyenga uja akali moyo ankati, ‘Patapita masiku atatu, ndidzaukanso.’

64Tsono mulamule kuti azilondapo pamanda pake mpaka mkucha. Tikuwopa kuti ophunzira ake angadzabwere nkudzaba mtembo wake, kenaka namadzauza anthu kuti ‘Iye uja wauka kwa akufa.’ Apo kunyenga kotsirizaku kudzakhala koipa zedi kupambana koyamba kuja.”

65Pilato adaŵauza kuti, “Paja alonda muli nawo. Pitani, kalondeni pamandapo monga mukudziŵira.”

66Iwo adapitadi, nakatseka manda kolimba posindikiza chizindikiro pa chimwala chotsekeracho. Kenaka adasiya asilikali akulonda pomwepo.

Blog
About Us
Message
Site Map

Who We AreWhat We EelieveWhat We Do

Terms of UsePrivacy Notice

2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.

Home
Gospel
Question
Blog
Help