2 Sam. 12 - Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Natani adzudzula Davide ndipo Davide alapa.

1 chifukwa Chauta adaamkonda.

Davide alanda mzinda wa Raba.(1 Mbi. 20.1-3)

26Nthaŵi imeneyo Yowabu ndi ankhondo a Aisraele ankathira nkhondo Raba, likulu la Aamoni, ndipo anali pafupi kuulanda.

27Adatuma amithenga kwa Davide kukamuuza kuti, “Ndauthira nkhondo mzinda wa Raba, ndipo ndalanda nkhokwe yake ya madzi.

28Tsono inu musonkhanitse ankhondo onse otsala, ndipo bwerani mudzauzinge ndi zithando mzindawo ndi kuulanda, kuwopa kuti ine ndikalanda mzindawo, ungamatchedwe dzina langa.”

29Choncho Davide adasonkhanitsa ankhondo ake onse, ndipo adapita ku Raba, nakauthira nkhondo mzindawo, nkuulanda.

30Tsono Davide adaivula chisoti kumutu mfumu ya Aamoni. Chisoticho chinkalemera makilogramu agolide, ndipo pa chisotipo panali mwala wamtengowapatali. Davide adachivala chisoticho, natenga zofunkha zochuluka mumzindamo.

31Adaŵatulutsa anthu amumzindamo, nakaŵagwiritsa ntchito ndi masowo ndi mapiki ndi nkhwangwa, ndi kuŵaumbitsa njerwa. Umu ndimo m'mene adachitira ndi mizinda yonse ya Aamoni. Pambuyo pake Davide adabwerera ku Yerusalemu pamodzi ndi ankhondo onse.

Blog
About Us
Message
Site Map

Who We AreWhat We EelieveWhat We Do

Terms of UsePrivacy Notice

2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.

Home
Gospel
Question
Blog
Help