Eks. 13 - Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Za kupereka mwana wachisamba kwa Chauta

1Chauta adauzanso Mose kuti,

2 Monsemo nkuti Aisraele ali okonzekeratu za nkhondo.

19Gen. 50.25; Yos. 24.32 Mose adanyamula mafupa aja a Yosefe, chifukwa Yosefeyo anali atalumbiritsa Aisraele aja kuti ndithu mafupawo adzanyamule. Paja Yosefe adaanena kuti, “Ndithu, Mulungu adzakuthandizani, koma mudzayenera kunyamula mafupa angaŵa kuchoka nawo kuno.”

20Aisraele adachoka ku Sukoti, nakagona ku Etamu m'mbali mwa chipululu.

21Nthaŵi yamasana Chauta ankaŵatsogolera ndi chipilala chamtambo namaŵalangiza njira. Ndipo nthaŵi yausiku, ankaŵatsogolera ndi chipilala chamoto, kuŵaunikira njira kuti aziyenda masana ndi usiku womwe.

22Lun. 10.17, 18; 18.3Nthaŵi zonse chipilala chamtambo chinkatsogolera anthu masana, ndipo chipilala chamoto chinkaŵatsogolera usiku.

Blog
About Us
Message
Site Map

Who We AreWhat We EelieveWhat We Do

Terms of UsePrivacy Notice

2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.

Home
Gospel
Question
Blog
Help