1Bwerani, mudzatamande Chauta,
Inu nonse atumiki a Chauta,
inu amene mumatumikira m'Nyumba mwake usiku.
2Kwezani manja anu popemphera m'malo ake oyera,
ndipo mutamande Chauta.
3Akudalitseni Chauta amene amakhala ku Ziyoni,
amene adalenga kumwamba ndi dziko lapansi.
Who We AreWhat We EelieveWhat We Do
2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.