2 Mbi. 36 - Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Yehowahazi, Yehoyakimu ndi Yehoyakini mafumu a ku Yuda(2 Maf. 23.30-35)

1Anthu am'dzikomo adatenga Yehowahazi mwana wa Yosiya, namlonga ufumu m'malo mwa atate ake ku Yerusalemu.

2Yehowahazi anali wa zaka 23 pamene ankaloŵa ufumu. Ndipo adalamulira miyezi itatu ku Yerusalemu.

3Pambuyo pake mfumu ya ku Ejipito idamchotsa Yehowahaziyo ku Yerusalemu, ndipo idakhometsa dziko msonkho wokwanira makilogramu 3,400 a siliva ndi 34 a golide.

4 amene sanachitike, akwaniritsidwe.”

Kirusi alola kuti aliyense wofuna abwerere kwao(Eza. 1.1-4)

22Tsono chaka choyamba cha ufumu wa Kirusi, mfumu ya ku Persiya, Chauta adautsa mtima wa Kirusiyo, kuti alengeze ku maiko onse a ufumu wake mpaka kulemba kumene. Adachita choncho kuti zimene Chauta adaalankhula kudzera mwa Yeremiya zipherezere. Adati,

23Yes. 44.28“Kirusi, mfumu ya ku Persiya, akunena kuti, ‘Chauta, Mulungu wakumwamba, wandipatsa ine maufumu onse pa dziko lapansi. Ndipo wandilamula kuti ndimmangire Nyumba ku Yerusalemu, ku Yuda. Aliyense mwa inu nonse amene ali munthu wa Chauta, Chauta Mulungu wakeyo akhale naye. Ndipo apite.’ ”

Blog
About Us
Message
Site Map

Who We AreWhat We EelieveWhat We Do

Terms of UsePrivacy Notice

2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.

Home
Gospel
Question
Blog
Help