2 PETRO Mau Oyamba - Buku Lopatulika ndilo Mau a Mulungu

Mau Oyamba Kalata yachiwiri ya Petro kwa gulu lalikulu la Akhristu oyambirira. Cholinga chenicheni cha kalatayi ndicho kulimbana ndi zonena za aphunzitsi onyenga ndi makhalidwe oipa amene amabwera chifukwa cha chiphunzitsochi. Yankho lake la mavutowa lipezeka pogwiritsitsa chidziwitso chenicheni cha Mulungu ndi cha Ambuye Yesu Khristu. Chidziwitso chimenechi chinaperekedwa ndi anthu amene iwo eni adamuona Yesu chamaso namumva iye akulalikira. Wolembayo akukhudzidwa makamaka ndi chiphunzitso chakuti Khristu sadzabweranso. Iye akunena kuti kuchedwa kubweranso kwa Khristu ndi chifukwa chakuti, “Ambuye sazengereza nalo lonjezano, monga ena achiyesa chizengerezo; komatu aleza mtima kwa inu, wosafuna kuti ena aonongeke, koma kuti onse afike kukulapa.” (3.9)Za mkatimuMau oyamba 1.1-2Maitanidwe a Chikhristu 1.3-21Aphunzitsi onyenga 2.1-22Kubweranso komaliza kwa Khristu 3.1-18
Blog
About Us
Message
Site Map

Who We AreWhat We EelieveWhat We Do

Terms of UsePrivacy Notice

2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.

Home
Gospel
Question
Blog
Help