ZEFANIYA Mau Oyamba - Buku Lopatulika ndilo Mau a Mulungu

Mau OyambaIyeyu adalalika mau ake pa nthawi imene mfumu Yosiya anali pafupi kukhazikitsa malamulo oongolera zinthu mu ufumu wake (621 BC.) Bukuli lili ndi mitu yosiyanasiyana ya mauthenga a uneneri monga: tsiku la chiweruzo ndi chiwonogeko, pamene Yuda adzalangidwe chifukwa chopembedza milungu ina. Yehova adzalanganso mitundu ina. Ngakhale Yerusalemu adzawonongeke, patsogolopo mzindawo udzakonzedwanso, ndipo anthu odzichepetsa ndi olungama adzakhala m'menemo.Za mkatimuZa tsiku la Yehova pamene Mulungu adzaimba mlandu 1.1—2.3

Tsoka lodzagwera mitundu ina ya anthu yozungulira Israele 2.4-15

Tsoka lodzagwera Yerusalemu; adzalapa ndipo Yehova adzamuwombola 3.1-20

Blog
About Us
Message
Site Map

Who We AreWhat We EelieveWhat We Do

Terms of UsePrivacy Notice

2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.

Home
Gospel
Question
Blog
Help