MASALIMO 53 - Buku Lopatulika ndilo Mau a Mulungu

Kupusa ndi kuipa kwa anthu(Mas. 14)Kwa Mkulu wa Nyimbo: pa Mahalati. Chilangizo cha Davide.

1

Pakubweretsa Mulungu anthu ake a m'ndende,

Yakobo adzakondwera, Israele adzasekera.

Blog
About Us
Message
Site Map

Who We AreWhat We EelieveWhat We Do

Terms of UsePrivacy Notice

2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.

Home
Gospel
Question
Blog
Help