1 Gen. 4.25-26 Adamu, Seti, Enosi,
2Kenani, Mahalalele, Yaredi,
3Enoki, Metusela, Lameki,
4Gen. 6.10Nowa, Semu, Hamu, ndi Yafeti.
5Ana a Yafeti: Gomeri, ndi Magogi, ndi Madai, ndi Yavani, ndi Tubala, ndi Meseki, ndi Tirasi.
6Ndi ana a Gomeri: Asikenazi, Difati, ndi Togarima.
7Ndi ana a Yavani: Elisa, ndi Tarisisi, Kitimu, ndi Rodanimu.
8 Gen. 10.6-20 Ana a Hamu: Kusi, ndi Ejipito, Puti, ndi Kanani.
9Ndi ana a Kusi: Seba, ndi Havila, ndi Sabita, ndi Raama, ndi Sabiteka. Ndi ana a Raama: Sheba, ndi Dedani.
10Ndi Kusi anabala Nimirodi; iye anayamba kukhala wamphamvu padziko.
11Ndi Ejipito anabala Aludi, ndi Aanamimu, ndi Alehabu, ndi Anafituhimu,
12ndi Apatirusi, ndi Akasiluhimu, (kumene anafuma Afilisti), ndi Akafitori.
13Ndi Kanani anabala Sidoni mwana wake woyamba, ndi Heti,
14ndi Ayebusi, ndi Aamori, ndi Agirigasi,
15ndi Ahivi, ndi Aariki, ndi Asini,
16ndi Aaravadi, ndi Azemari, ndi Ahamati.
17Ana a Semu: Elamu, ndi Asiriya, ndi Aripakisadi, ndi Ludi, ndi Aramu, ndi Uzi, ndi Huli, ndi Getere, ndi Meseki.
18Ndi Aripakisadi anabala Sela; ndi Sela anabala Eberi.
19Ndi Eberi anabala ana aamuna awiri, dzina la winayo ndiye Pelegi, popeza masiku ake dziko linagawanika; ndi dzina la mbale wake ndiye Yokotani.
20Ndipo Yokotani anabala Alimodadi, ndi Selefi, ndi Hazara-Maveti, ndi Yera;
21ndi Hadoramu, ndi Uzali, ndi Dikila;
22ndi Ebala, ndi Abimaele, ndi Sheba,
23ndi Ofiri, ndi Havila, ndi Yobabu. Awa onse ndiwo ana a Yokotani.
Makolo kuyambira Semu mpaka adzukulu a Abrahamu24Semu, Aripakisadi, Sela;
25Eberi, Pelegi, Reu,
26Serugi, Nahori, Tera;
27Gen. 17.5Abramu, (ndiye Abrahamu).
28Gen. 16.11; 21.2Ana a Abrahamu: Isaki, ndi Ismaele.
Mbumba ya Ismaele(Gen. 25.12-16)29Mibadwo yao ndi awa; woyamba wa Ismaele Nebayoti; ndi Kedara ndi Adibeele, ndi Mibisamu,
30Misima, ndi Duma, Masa, Hadadi, ndi Tema,
31Yeturi, Nafisi, ndi Kedema. Awa ndi ana a Ismaele.
32Ndi ana a Ketura mkazi wamng'ono wa Abrahamu anabala Zimirani, ndi Yokisani, ndi Medani, ndi Midiyani, ndi Isibaki, ndi Suwa. Ndi ana a Yokisani: Sheba, ndi Dedani.
33Ndi ana a Midiyani: Efa, ndi Efere, ndi Hanoki, ndi Abida, ndi Elida. Awa onse ndiwo ana a Ketura.
Mbumba ya Esau(Gen. 36.1-19)34 Gen. 25.25-26; 32.28 Ndipo Abrahamu anabala Isaki. Ana a Isaki: Esau, ndi Israele.
35Ana a Esau: Elifazi, Reuwele, ndi Yeusi, ndi Yalamu, ndi Kora.
36Ana a Elifazi: Temani, ndi Omara, Zefi, ndi Gatamu, Kenazi, ndi Timna, ndi Amaleke.
37Ana a Reuwele: Nahati, Zera, Sama, ndi Miza.
38Ndi ana a Seiri: Lotani, ndi Sobala, ndi Zibiyoni, ndi Ana, ndi Disoni, ndi Ezere, ndi Disani.
39Ndi ana a Lotani: Hori, ndi Homamu; ndipo Timna ndiye mlongo wake wa Lotani.
40Ana a Sobala: Aliyani, ndi Manahati, ndi Ebala, Sefi, ndi Onamu. Ndi ana a Zibiyoni: Aiya ndi Ana.
41Mwana wa Ana: Disoni. Ndi ana a Disoni: Hamurani, ndi Esibani, ndi Itirani, ndi Kerani.
42Ana a Ezere: Bilihani, ndi Zaavani, ndi Yaakani. Ana a Disani: Uzi, ndi Arani.
43Gen. 36.31Mafumu tsono akuchita ufumu m'dziko la Edomu, pakalibe mfumu wakuchita ufumu pa ana a Israele, ndiwo Bela mwana wa Beori; ndi dzina la mzinda wake ndilo Dinihaba.
44Ndipo anafa Bela; ndi Yobabu mwana wa Zera wa ku Bozira anakhala mfumu m'malo mwake.
45Namwalira Yobabu; ndi Husamu wa ku dziko la Atemani anakhala mfumu m'malo mwake.
46Namwalira Husamu; ndi Hadadi mwana wa Bedadi, amene anakantha Midiyani ku thengo la Mowabu, anakhala mfumu m'malo mwake; ndi dzina la mzinda wake ndi Aviti.
47Namwalira Hadadi; ndi Samila wa ku Masireka anakhala mfumu m'malo mwake.
48Namwalira Samila: ndi Shaulo wa ku Rehoboti ku nyanja anakhala mfumu m'malo mwake.
49Namwalira Shaulo; ndi Baala-Hanani mwana wa Akibori anakhala mfumu m'malo mwake.
50Namwalira Baala-Hanani; ndi Hadadi anakhala mfumu m'malo mwake; ndipo dzina la mzinda wake ndi Pai; ndi dzina la mkazi wake ndiye Mehetabele mwana wamkazi wa Matiredi mwana wamkazi wa Mezahabu.
51Namwalira Hadadi. Ndipo mafumu a Edomu ndiwo mfumu Timna, mfumu Aliva, mfumu Yeteti;
52mfumu Oholibama, mfumu Ela, mfumu Pinoni;
53mfumu Kenazi, mfumu Temani, mfumu Mibizara;
54mfumu Magadiele, mfumu Iramu. Awa ndi mafumu a Edomu.
Who We AreWhat We EelieveWhat We Do
2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.