1Mwananga, sunga mau anga,
ukundike malangizo anga,
2
ndi chisiyo ndi sinamoni.
18Tiye tikondwere ndi chikondano mpaka mamawa;
tidzisangalatse ndi chiyanjano.
19Pakuti mwamuna kulibe kwathu,
wapita ulendo wa kutali;
20watenga thumba la ndalama m'dzanja lake,
tsiku lowala mwezi adzabwera kwathu.
21Amkakamiza ndi kukoka kwa mau ake,
ampatutsa ndi kusyasyalika kwa milomo yake.
22Mnyamatayo amtsata posachedwa,
monga ng'ombe ipita kukaphedwa;
ndi monga unyolo umadza kulanga chitsiru;
23 Mlal. 9.12 mpaka muvi ukapyoza mphafa yake;
amtsata monga mbalame yothamangira msampha;
osadziwa kuti adzaononga moyo wake.
24Ndipo tsopano, ananga, mundimvere ine,
labadirani mau a m'kamwa mwanga.
25Mtima wako usapatukire kunjira ya mkaziyo,
usasochere m'mayendedwe ake.
26 Neh. 13.26 Pakuti amagwetsa ambiri, atawalasa;
ndipo ophedwa ndi iye achulukadi.
27Nyumba yake ndiyo njira ya kumanda,
yotsikira kuzipinda za imfa.
Who We AreWhat We EelieveWhat We Do
2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.