MALIRO Mau Oyamba - Buku Lopatulika ndilo Mau a Mulungu

Mau OyambaMau a m'bukuli ali ngati ndakatulo zolira chifukwa cha kupasuka kwa Yerusalemu ndi mavuto aakulu a ukapolo, zimene zidachitika m'chaka cha 586 BC. Mau ake ndi achisoni ndi odandaula, komabe mauwo aonetsanso mtima wokhulupirira Mulungu poyembekeza kuti adzakhalanso pabwino nthawi yake itakwana. Ayuda akhala akugwiritsabe ntchito ndakatulo zimenezi pa chipembedzo mpaka lero, pa masiku okumbukira kupasuka kwa mzinda wa Yerusalemu m'chaka cha 586 BC.Za mkatimuZomumvetsa chisoni Yerusalemu 1.1-22

Chilango chogwera mzindawo 2.1-22

Yerusalemu azunzika, alapa ndipo ayembekeza chikhululukiro 3.1-66

Yerusalemu wasanduka bwinja 4.1-22

Pemphero lopempha chikhululukiro 5.1-22

Blog
About Us
Message
Site Map

Who We AreWhat We EelieveWhat We Do

Terms of UsePrivacy Notice

2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.

Home
Gospel
Question
Blog
Help