NAHUMU Mau Oyamba - Buku Lopatulika ndilo Mau a Mulungu
Mau OyambaBukuli ndi ndakatulo yokondwerera kupasuka kwa Ninive, mzinda waukulu wa Aasiriya amene ankazunza Aisraele kuyambira kale. Kupasuka kwa mzindawo kuwoneka ngati chilango cha Mulungu chogwera anthu onyada ndi ankhanza.Za mkatimuChauta aimba Ninive mlandu 1.1-15 Kupasuka kwa mzindawo 2.1—3.19