HAGAI Mau Oyamba - Buku Lopatulika ndilo Mau a Mulungu

Mau OyambaMneneriyu adalalika mau ake chaka cha 520 BC., Ayuda ena atabwerera ku Yerusalemu kuchokera ku ukapolo. Anthuwo anali atabwerera ku ukapolo namakhala ku Yerusalemu kwa zaka zingapo, koma Kachisi anali bwinja lenileni. Atsogoleri anapereka uthenga kwa anthu kuti amangenso Kachisi, ndipo Ambuye akulonjeza kuti m'tsogolo anthu ake adzakhala pabwino ndi pa mtendere.Za mkatimuYehova awalamula kuti amangenso Nyumba yake 1.1-15

Mau ena owalimbitsa mtima Ayudawo 2.1-23

Blog
About Us
Message
Site Map

Who We AreWhat We EelieveWhat We Do

Terms of UsePrivacy Notice

2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.

Home
Gospel
Question
Blog
Help