NYIMBO YA SOLOMONI Mau Oyamba - Buku Lopatulika ndilo Mau a Mulungu

Mau Oyamba Nyimbo ya Solomoni ndi mndandanda wa ndakatulo za chikondi, ndipo zambiri mwa izo zili ngati nyimbo zimene mwamuna amalankhula kwa mkazi, kapena mkazi kwa mwamuna. Ambiri amakhulupirira kuti Solomoni ndiye analemba nyimboyi.Ayuda amakhulupirira kuti nyimbozi zikuonetsa za ubale wa Mulungu ndi anthu ake, pamene Akhristu amakhulupirira kuti zikuonetsa za ubale wa Yesu ndi mpingo. Nyimbo zake zilipo zisanu ndi imodzi.Za mkatimuNyimbo yoyamba 1.1—2.7

Nyimbo yachiwiri 2.8—3.5

Nyimbo yachitatu 3.6—5.1

Nyimbo yachinai 5.2—6.3

Nyimbo yachisanu 6.4—8.4

Nyimbo yachisanu ndi chimodzi 8.5-14

Blog
About Us
Message
Site Map

Who We AreWhat We EelieveWhat We Do

Terms of UsePrivacy Notice

2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.

Home
Gospel
Question
Blog
Help