1 1Mbi. 9.33 Taonani, lemekezani Yehova, atumiki a Yehova inu nonse,
akuimirira m'nyumba ya Yehova usiku.
2 1Tim. 2.8 Kwezani manja anu kumalo oyera,
nimulemekeze Yehova.
3 Mas. 128.5 Yehova, ali mu Ziyoni, akudalitseni;
ndiye amene analenga kumwamba ndi dziko lapansi.
Who We AreWhat We EelieveWhat We Do
2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.