MALAKI Mau Oyamba - Buku Lopatulika ndilo Mau a Mulungu

Mau OyambaMneneri Malaki adalalikira nthawi imene Ayuda anali atamanganso Kachisi wa Yehova ku Yerusalemu. Iye analangiza ansembe ndi anthu ao, kuti adziperekenso kwa Yehova ndi kumamutumikira mokhulupirika, ndi kuti apewe ziphuphu, zachiphamaso ndi kunyenga kulikonse, ndipo asamale za chipembedzo.Ansembe ndi anthu ena amachita chinyengo pa zopereka zao kwa Mulungu, ndipo samatsana chiphunzitso cha Mulungu.Mneneriyo anawauzanso kuti lidzafika tsiku limene Yehova adzabwera kudzazenga mlandu ndi kuyeretsa anthu ake, ndipo adachita izi potumiza wamthenga wake kuti akakonze njira ndi kunenera za chipangano chake.Za mkatimuKuchimwa kwa Aisraele pa zinthu zina ndi zina 1.1—2.16

Yehova akubwera kudzaweruza ndi kuyeretsa anthu ake 2.17—4.6

Blog
About Us
Message
Site Map

Who We AreWhat We EelieveWhat We Do

Terms of UsePrivacy Notice

2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.

Home
Gospel
Question
Blog
Help