1 Aro. 12.16 Yehova, mtima wanga sunadzikuze
ndi maso anga sanakwezeke;
ndipo sindinatsate zazikulu,
kapena zodabwitsa zondiposa.
2 Mat. 18.3; 1Ako. 14.20 Indedi, ndinalinganiza ndi kutontholetsa moyo wanga;
ngati mwana womletsa kuyamwa amake,
moyo wanga ndili nao ngati mwana womletsa kuyamwa.
3Israele, uyembekezere Yehova,
kuyambira tsopano kufikira kosatha.
Who We AreWhat We EelieveWhat We Do
2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.