1Ndipo chizindikiro chachikulu chinaoneka m'mwamba; mkazi wovekedwa dzuwa, ndi mwezi kumapazi ake, ndi pamutu pake korona wa nyenyezi khumi ndi ziwiri;
2ndipo anali ndi pakati; ndipo afuula alimkubala, ndi kumva zowawa zakubala.
3
Who We AreWhat We EelieveWhat We Do
2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.