1
18 1Tim. 4.14 Lamulo ili ndipereka kwa iwe, mwana wanga Timoteo, kuti, monga mwa zonenera zidakutsogolera iwe kale, ulimbane nayo nkhondo yabwino;
191Tim. 3.9; 6.9ndi kukhala nacho chikhulupiriro ndi chikumbu mtima chokoma, chimene ena adachikankha, chikhulupiriro chao chidatayika;
201Ako. 5.5; 2Tim. 4.14a iwo ali Himeneo ndi Aleksandro, amene ndawapereka kwa Satana, kuti aphunzire kusalankhula zamwano.
Who We AreWhat We EelieveWhat We Do
2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.