MASALIMO 11 - Buku Lopatulika Bible 2014
Yehova asunga anthu ake nalanga oipaKwa Mkulu wa Nyimbo; Salimo la Davide.
1
ndi mphepo yoopsa zidzawagawikira m'chikho chao.
7 Mas. 45.7; 1Yoh. 3.2 Pakuti Yehova ndiye wolungama; akonda zolungama;
woongoka mtima adzapenya nkhope yake.