2 TIMOTEO 4 - Buku Lopatulika Bible 2014

1

19 Mac. 18.2; 2Tim. 1.16 Pereka moni kwa Prisika ndi Akwila, ndi banja la Onesifore.

20Mac. 19.22; 21.29Erasto anakhalira m'Korinto; koma Trofimo ndamsiya wodwala ku Mileto.

212Tim. 4.9Tayesetsa kudza isanadze nyengo yachisanu. Akukupatsa moni Yubulo, ndi Pude, ndi Lino, ndi Klaudia, ndi abale onse.

22 Agal. 6.18 Ambuye akhale ndi mzimu wako. Chisomo chikhale nanu.

Blog
About Us
Message
Site Map

Who We AreWhat We EelieveWhat We Do

Terms of UsePrivacy Notice

2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.

Home
Gospel
Question
Blog
Help