3 YOHANE Mau Oyamba - Buku Lopatulika Bible 2014
Mau Oyamba Kalata yachitatu yolembedwa ndi mtumwi Yohane inalembedwa ndi “Mkuluyo” kulembera mtsogoleri wa mpingo dzina lake Gayo. Mlembiyo akumuyamikira Gayo chifukwa cha kuthandiza akhristu ena, komanso akuwachenjeza za munthu wina dzina lake Diotrefe.Za mkatimuMau oyamba 1.1-4Gayo akumulemekeza 1.5-8Diotrefe akumudzudzula 9-10Demetrio akumuyamikira 1.11-12Mau omaliza 1.13-15