1Pemphero la Habakuku mneneri, pa Sigionoti.
2
ndi mapiri achikhalire anamwazika,
zitunda za kale lomwe zinawerama;
mayendedwe ake ndiwo a kale lomwe.
7Ndinaona mahema a Kusani ali mkusauka;
nsalu zotchinga za dziko la Midiyani zinanjenjemera.
8Kodi Yehova anaipidwa nayo mitsinje?
Mkwiyo wanu unali pamitsinje kodi,
kapena ukali wanu panyanja,
kuti munayenda pa akavalo anu,
pa magaleta anu a chipulumutso?
9
ndi m'minda m'mosapatsa chakudya;
ndi zoweta zachotsedwa kukhola,
palibenso ng'ombe m'makola mwao;
18 Yob. 13.15; Yes. 61.10 koma ndidzakondwera mwa Yehova,
ndidzasekerera mwa Mulungu wa chipulumutso changa.
19 Mas. 27.1 Yehova, Ambuye, ndiye mphamvu yanga,
asanduliza mapazi anga ngati a mbawala,
nadzandipondetsa pa misanje yanga.
Who We AreWhat We EelieveWhat We Do
2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.