MARKO 9 - Buku Lopatulika Bible 2014

Mawalitsidwe a Yesu paphiri(Mat. 17.1-13; Luk. 9.28-36)

1

45Ndipo ngati phazi lako likulakwitsa, ulidule; kulowa iwe m'moyo wopunduka mwendo, kuli kwabwino koposa ndi kukhala ndi mapazi ako awiri ndi kuponyedwa m'Gehena.

47Mat. 5.29; 18.8-9Ndipo ngati diso lako likulakwitsa ulikolowole; kulowa iwe m'Ufumu wa Mulungu ndi diso limodzi kuli kwabwino koposa ndi kukhala ndi maso awiri ndi kuponyedwa m'Gehena;

48kumeneko mphutsi yao siikufa, ndi moto suzimidwa.

49Pakuti onse adzathiridwa mchere wamoto.

50Mat. 5.13; Luk. 14.34; Aro. 12.18; 2Ako. 13.11; Akol. 4.6; Aheb. 12.14Mchere uli wabwino; koma ngati mchere unasukuluka, mudzaukoleretsa ndi chiyani? Khalani nao mchere mwa inu nokha, ndipo khalani ndi mtendere wina ndi mnzake.

Blog
About Us
Message
Site Map

Who We AreWhat We EelieveWhat We Do

Terms of UsePrivacy Notice

2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.

Home
Gospel
Question
Blog
Help