2 MBIRI Mau Oyamba - Buku Lopatulika Bible 2014
Mau OyambaBukuli likamba za mfumu Solomoni ndi mafumu a ku Yuda okha mpaka nthawi ya kupasuka kwa mzinda wa Yerusalemu.Za mkatimuUfumu wa Solomoni 1.1—9.31a. Zaka zoyamba za ufumu wake 1.1-17 b. Amanga Kachisi wa Yehova 2.1—7.10 c. Zaka zotsiriza za ufumu wake 7.11—9.31 Za mafumu ena a ku Yuda 10.1—36.23a. Mafumu akumpoto aukira ufumu wa Rehobowamu 10.1-19b. Mafumu a ku Yuda 11.1—36.12c. Kupasuka kwa mzinda wa Yerusalemu 36.13-23