FILEMONI Mau Oyamba - Buku Lopatulika Bible 2014
Mau OyambaFilemoni anali mkhristu wodziwika bwino, makamaka mu mpingo wa ku Kolose. Iye anali ndi kapolo wake dzina lake Onesimo amene adamthawa. Tsiku lina Onesimoyo adakumana ndi Paulo, nthawi imeneyo nkuti Pauloyo ali m'ndende, ndipo kudzera mwa Pauloyo, Onesimo anasanduka mkhristu. Paulo akumulembera kalata Filemoni uti amchitire chifundo kapolo wakeyo, ndipo amulandire ngati mbale wake mwa Khristu.Za mkatimuMau oyamba 1.1-3Ayamba wayamikira chikondi chake ndi chikhulupiriro chake 1.4-7Paulo amnenera Onesimo 1.8-22Mau omaliza 1.23-25