1
8Chotsalira, abale, zinthu zilizonse zoona, zilizonse zolemekezeka, zilizonse zolungama, zilizonse zoyera, zilizonse zokongola, zilizonse zimveka zokoma; ngati kuli chokoma mtima china, kapena chitamando china, zilingirireni izi.
9
21 Agal. 1.2 Lankhulani woyera mtima aliyense mwa Khristu Yesu. Abalewo akukhala ndi ine alankhula inu.
22Afi. 1.13Oyera mtima onse alankhula inu, koma makamaka iwo a banja la Kaisara.
23Chisomo cha Ambuye Yesu Khristu chikhale ndi mzimu wanu.
Who We AreWhat We EelieveWhat We Do
2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.