1
12 1Ako. 15.1; 2Ako. 1.19 Mwa Silivano, mbale wathu wokhulupirika monga ndimayesa, ndalembera kwa inu mwachidule, ndi kudandaulira, ndi kuchita umboni, kuti chisomo choona cha Mulungu ndi ichi; m'chimenechi muimemo.
13Mac. 12.12, 25Iye wa ku Babiloni wosankhidwa pamodzi nanu akulankhulani; ateronso Marko mwana wanga.
14Aro. 16.16; Aef. 6.23Mupatsane moni ndi chipsompsono cha chikondi.
Mtendere ukhale ndi inu nonse muli mwa Khristu.
Who We AreWhat We EelieveWhat We Do
2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.