MASALIMO 68 - Buku Lopatulika Bible 2014

Mau akuyamikira Mulungu wa chipulumutso chonseKwa Mkulu wa Nyimbo. Salimo la Davide. Nyimbo.

1

ndi nthenga zake zokulira ndi golide woyenga wonyezimira.

14Pamene Wamphamvuyonse anabalalitsa mafumu m'dzikomo,

munayera ngati matalala m'Zalimoni.

15Phiri la Basani ndilo phiri la Mulungu;

Phiri la Basani ndilo phiri la mitumitu.

16Muchitiranji nsanje mapiri inu a mitumitu,

ndi phirilo Mulungu analikhumba, akhaleko?

Inde, Yehova adzakhalabe komweko kosatha.

17

mafumu adzabwera nacho chaufulu kukupatsani.

30Dzudzulani chilombo cha m'bango,

khamu la mphongo ndi ng'ombe za anthu,

yense wakudzigonjera ndi ndalama za siliva;

anabalalitsa mitundu ya anthu ya kukondwera nayo nkhondo.

31 Yes. 19.19, 21; 43.3 Akulu adzafumira ku Ejipito;

Kusi adzafulumira kutambalitsa manja ake kwa Mulungu.

32Imbirani Mulungu, maufumu a dziko lapansi inu;

imbirani Ambuye zomlemekeza.

33Kwa Iye wakuberekeka pamwambamwamba,

oyambira kale lomwe;

taonani; amveketsa liu lake, ndilo liu lamphamvu.

34Vomerezani kuti mphamvu nja Mulungu;

ukulu wake uli pa Israele,

ndi mphamvu yake m'mitambo.

35 Mas. 45.3-4 Inu Mulungu, ndinu woopsa m'malo oyera anu;

Mulungu wa Israele ndiye amene apatsa anthu ake

mphamvu ndi chilimbiko.

Alemekezeke Mulungu.

Blog
About Us
Message
Site Map

Who We AreWhat We EelieveWhat We Do

Terms of UsePrivacy Notice

2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.

Home
Gospel
Question
Blog
Help