RUTE Mau Oyamba - Buku Lopatulika Bible 2014
Mau OyambaBukuli likamba nkhani ya Rute, mkazi wachimowabu amene adakwatiwa ndi mwamuna wa ku Israele. Mwamuna wake atamwalira, iye atsatira mpongozi wake Naomi ku Betelehemu kwao chifukwa chokhulupirira Mulungu mwa Aisraele.Nkhani yabwinoyi yochitika panthawi yankhanza ya Oweruza ija, iwonetsa kuti ngakhale amitundu nawonso adzalandira madalitso a Mulungu, akakhulupirika Mulungu wa Israele ndi kusanduka anthu ake.Za mkatimuNaomi abwerera ku Betelehemu pamodzi ndi Rute 1.1-22Rute akumana ndi Bowazi 2.1—3.18Rute akwatiwa ndi Bowazi Davide 4.1-22