MASALIMO 74 - Buku Lopatulika Bible 2014

Malo oyera adetsedwa. Apempha Mulungu akumbuke chipangano chaoChilangizo cha Asafu.

1

ndipo mwa ife palibe wina wakudziwa mpaka liti.

10Wotsutsanayo adzatonza kufikira liti, Mulungu?

Kodi mdani adzanyoza dzina lanu nthawi yonse?

11Mubwezeranji dzanja lanu, ndilo dzanja lamanja lanu?

Mulitulutse kuchifuwa chanu ndipo muwatheretu.

12

mudampereka akhale chakudya cha zilombo za m'chipululu.

15 Yos. 3.13-17 Mudagawa kasupe ndi mtsinje;

mudaphwetsa mitsinje yaikulu.

16 Gen. 1.14-19 Usana ndi wanu, usikunso ndi wanu,

munakonza kuunika ndi dzuwa.

17 Gen. 8.22 Munaika malekezero onse a dziko lapansi;

munalenga dzinja ndi malimwe.

18Mukumbukire ichi, Yehova, mdaniyo anatonza,

ndipo anthu opusa ananyoza dzina lanu.

19Musapereke moyo wa njiwa yanu kwa chilombo;

musamaiwala moyo wa ozunzika anu nthawi yonse.

20 Gen. 17.7; Yer. 33.20-21 Samalirani chipanganocho;

pakuti malo a mdima a m'dziko adzala ndi zokhalamo chiwawa.

21Okhalira mphanthi asabwere nao manyazi;

wozunzika ndi waumphawi alemekeze dzina lanu.

22Nyamukani, Mulungu, mudzinenere mlandu nokha;

kumbukirani momwe akutonzani wopusa tsiku lonse.

23Musaiwale mau a iwo otsutsana ndi Inu;

kusokosera kwa iwo akuukirani Inu kumakwera kosaleka.

Blog
About Us
Message
Site Map

Who We AreWhat We EelieveWhat We Do

Terms of UsePrivacy Notice

2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.

Home
Gospel
Question
Blog
Help