1Ndipo Mose ndi akulu a Israele anauza anthu, nati, Sungani malamulo onse ndikuuzani lero.
2
16
17 Deut. 19.14 Wotembereredwa iye wakusendeza malire a mnansi wake. Ndi anthu onse anene, Amen.
18 Lev. 19.14 Wotembereredwa wakusokeretsa wakhungu m'njira. Ndi anthu onse anene, Amen.
19 Eks. 22.21 Wotembereredwa iye wakuipsa mlandu wa mlendo, mwana wamasiye, ndi mkazi wamasiye. Ndi anthu onse anene, Amen.
20 Lev. 18.8 Wotembereredwa iye wakugona ndi mkazi wa atate wake; popeza wavula atate wake. Ndi anthu onse anene, Amen.
21 Lev. 18.23 Wotembereredwa iye wakugona ndi nyama iliyonse. Ndi anthu onse anene, Amen.
22 Lev. 18.9 Wotembereredwa iye wakugona ndi mlongo wake, mwana wamkazi wa atate wake, kapena mwana wamkazi wa make. Ndi anthu onse anene, Amen.
23 Lev. 18.17 Wotembereredwa iye wakugona ndi mpongozi wake. Ndi anthu onse anene, Amen.
24 Deut. 19.11 Wotembereredwa iye wakukantha mnansi wake m'tseri. Ndi anthu onse anene, Amen.
25 Eks. 23.7, 8 Wotembereredwa iye wakulandira chamwazi chakuti akanthe munthu wosachimwa. Ndi anthu onse anene, Amen.
26 Agal. 3.10 Wotembereredwa iye wosavomereza mau a chilamulo ichi kuwachita. Ndi anthu onse anene, Amen.
Who We AreWhat We EelieveWhat We Do
2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.