MACHITIDWE A ATUMWI 15 - Buku Lopatulika Bible 2014

Ku Yerusalemu atumwi ndi akulu aweruza za mdulidwe ndi Malamulo a Mose

1

35Mac. 13.1Koma Paulo ndi Barnabasi anakhalabe m'Antiokeya, nalinkuphunzitsa, ndi kulalikira mau a Ambuye pamodzi ndi ena ambiri.

Paulo ndi Barnabasi alekana

36 Mac. 13—14 Patapita masiku, Paulo anati kwa Barnabasi, Tibwerenso, tizonde abale m'midzi yonse m'mene tinalalikiramo mau a Ambuye, tione mkhalidwe wao.

37Mac. 12.12, 25; 13.5, 13; 2Tim. 4.11Ndipo Barnabasi anafuna kumtenga Yohane uja, wotchedwa Marko

38Koma sikunamkomera Paulo kumtenga iye amene anawasiya nabwerera pa Pamfiliya paja osamuka nao kuntchito.

39Ndipo panali kupsetsana mtima, kotero kuti analekana wina ndi mnzake; ndipo Barnabasi anatenga Marko, nalowa m'ngalawa, nanka ku Kipro.

Ulendo wachiwiri wa Paulo

40 Mac. 14.26 Koma Paulo anasankha Silasi, namuka, woikizidwa ndi abale ku chisomo cha Ambuye.

41Mac. 16.5Ndipo iye anapita kupyola pa Siriya ndi Silisiya, nakhazikitsa Mipingo.

Blog
About Us
Message
Site Map

Who We AreWhat We EelieveWhat We Do

Terms of UsePrivacy Notice

2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.

Home
Gospel
Question
Blog
Help