MASALIMO 110 - Buku Lopatulika Bible 2014
Ufumu wa AmbuyeSalimo la Davide.
1
chitani ufumu pakati pa adani anu.
3
5
adzadzaza dziko ndi mitembo;
adzaphwanya mitu m'maiko ambiri.
7 Ower. 7.5-6 Adzamwa kumtsinje wa panjira;
chifukwa chake adzaweramutsa mutu wake.