1
6Popyola chigwa cha kulira misozi achiyesa cha akasupe;
inde mvula ya chizimalupsa ichidzaza ndi madalitso.
7
8Yehova Mulungu wa makamu, imvani pemphero langa.
Tcherani khutu, Mulungu wa Yakobo.
9 Gen. 15.1 Onani, Mulungu, ndinu chikopa chathu;
ndipo penyani pa nkhope ya Wodzozedwa wanu.
10Pakuti tsiku limodzi m'mabwalo anu likoma
koposa masiku ambirimbiri akukhala pena.
Kukhala ine wapakhomo m'nyumba ya Mulungu wanga,
kundikonda ine koposa kugonera m'mahema a choipa.
11 Yes. 60.19-20; Mat. 6.33; 7.11 Pakuti Yehova Mulungu ndiye dzuwa ndi chikopa;
Yehova adzapatsa chifundo ndi ulemerero;
sadzakaniza chokoma iwo akuyenda angwiro.
12 Mas. 2.12 Yehova wa makamu,
wodala munthu wakukhulupirira Inu.
Who We AreWhat We EelieveWhat We Do
2025 by iamachristian.org,Inc All rights reserved.